Malachi 1:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Koma inuyo mumalinyoza ponena kuti tebulo la Chauta nlachabechabe, ndipo chakudya chopereka pamenepo nchonyozeka.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma inu muliipsa, pakunena inu, Gome la Yehova laipsidwa, ndi zipatso zake, chakudya chake, chonyozeka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma inu mumalinyoza ponena kuti tebulo la Ambuye, ‘ndi lodetsedwa,’ ndipo chakudya chake, ‘nʼchonyozeka!’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma inu muliipsa, pakunena inu, Gome la Yehova laipsidwa, ndi zipatso zace, cakudya cace, conyozeka.