Malachi 1:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akuti, “Ndakukondani inu.” Koma inu mumati. “Kodi mwatikonda motani?” Chauta akunena kuti, “Kodi suja Esau ndi mbale wake wa Yakobe?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndakukondani, ati Yehova; koma inu mukuti, Mwatikonda motani? Esau si mkulu wake wa Yakobo kodi? Ati Yehova; ndipo ndinakonda Yakobo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova akuti, “Ine ndakukondani. Koma inu mukufunsa kuti, ‘Kodi mwatikonda motani?’ ” Yehova akuti, “Kodi Esau sanali mʼbale wake wa Yakobo? Komatu Ine ndinakonda Yakobo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndakukondani, ati Yehova; koma inu mukuti, Mwatikonda motani? Esau si mkulu wace wa Yakobo kodi? ati Yehova; ndipo ndinakonda Yakobo;