Malachi 1:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu, Aisraele, mudzaziwona zimenezi ndi maso anu. Inu nomwe mudzati, “Ukulu wa Chauta umafika ngakhale kunja kwa malire a Aisraele.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo maso anu adzaona, nimudzati, Yehova ali wamkulu kupitirira malire a Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mudzaziona zimenezi ndi maso anu ndipo mudzati, ‘Yehova ndi Wamkulu, ukulu wake umafika ngakhale kunja kwa malire a Israeli!’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo maso anu adzaona, nimudzati, Yehova ali wamkuru kupitirira malire a Israyeli.