Malachi 3:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akunena kuti, “Mwalankhula mau olasa onena Ine. Komabe mukuti, ‘Kodi takunenani zotani?’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mau anu andilimbira, ati Yehova. Koma inu mukuti, Tanena motsutsana nanu ndi chiyani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova akuti, “Mwayankhula mawu owawa onena za Ine. “Komabe inu mukufunsa kuti, ‘Kodi tanena chiyani chotsutsana nanu?’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mau anu andilimbira, ati Yehova. Koma inu mukuti, Tanena motsutsana nanu ndi ciani?