Malachi 3:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ife timayesa kuti anthu odzikuza ndiwo odala. Anthu ochita zoipa ndiwo amene amakhala pabwino, ngakhale akaputa Mulungu amapulumuka ndithu.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsopano tiwatcha odzikuza odala, inde iwo ochita zoipa amangidwa ngati nyumba; inde, ayesa Mulungu, napulumuka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma tsono ife timati anthu odzikuza ndiye odalitsika. Kunena zoona anthu oyipa ndiye amapeza bwino, ngakhale amene amanyoza Mulungu amapulumuka.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsopano tiwacha odzikuza odala, inde iwo ocita zoipa amangidwa ngati nyumba; inde, ayesa Mulungu, napulumuka.