Malachi 3:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo mudzaonanso kusiyana pakati pa anthu abwino ndi anthu oipa, pakati pa anthu otumikira Mulungu ndi osamtumikira.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mudzabwera ndi kuzindikira pakati pa wolungama ndi woipa, pakati pa iye wotumikira Mulungu ndi iye wosamtumikira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo mudzaonanso kusiyana pakati pa anthu olungama ndi oyipa, pakati pa amene amatumikira Mulungu ndi amene satumikira Mulungu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mudzabwera ndi kuzindikira pakati pa wolungama ndi woipa, pakati pa iye wotumikira Mulungu ndi iye wosamtumikira.