Mark 1:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atapitirira pang'ono, Yesu adaona Yakobe ndi Yohane, ana a Zebedeo. Iwowo anali m'chombo, akukonza makoka ao,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo atapita patsogolo pang'ono, anaona Yakobo, mwana wa Zebedeo, ndi Yohane mbale wake, iwonso anali m'chombo nakonza makoka ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atapita patsogolo pangʼono, anaona Yakobo ndi mʼbale wake Yohane ana a Zebedayo, ali mʼbwato akukonza makoka awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo atapita patsogolo pang'ono, anaona Yakobo, mwana wa Zebedayo, ndi Yohane mbale wace, iwonso anali m'combo nakonza makoka ao.