Mark 1:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Udayamba monga mneneri Yesaya adalembera m'buku mwake kuti, “Mulungu akuti, “Ndidzatuma wamthenga wanga m'tsogolo mwako kuti akakonzeretu njira yoti iwe udzapitemo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga mwalembedwa m'Yesaya mneneri, Ona, ndituma mthenga wanga patsogolo pa nkhope yanu, amene adzakonza njira yanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
monga zalembedwera mʼbuku la mneneri Yesaya: “Ine ndidzatuma mthenga wanga patsogolo panu, amene adzakonza njira yanu,”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga mwalembedwa m'Yesaya mneneri, Ona, ndituma mthenga wanga patsogolo pa nkhope yanu, Amene adzakonza njira yanu;