Mark 10:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chimodzimodzinso ngati mkazi asudzula mwamuna wake, kenaka nkukwatiwa ndi wina, nayenso akuchita chigololo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo ngati mkazi akachotsa mwamuna wake, nakwatiwa ndi wina, achita chigololo iyeyu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo akasiya mwamuna wake ndi kukakwatiwa ndi wina, achita chigololo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo ngati mkazi akacotsa mwamuna wace, nakwatiwa ndi wina, acita cigololo iyeyu.