Mark 10:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atatero adayamba kuŵafungata anawo, naŵasanjika manja ndi kuŵadalitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Iye anatiyangata, natidalitsa, ndi kuika manja ake pa ito.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ananyamula ana mʼmanja ake, ndi kuyika manja ake pa iwo nawadalitsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Iye anatiyangata, natidalitsa, ndi kuika manja ace pa ito.