Mark 10:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu uja adati, “Aphunzitsi, zonsezi ndakhala ndikuzitsata kuyambira ndili mwana.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iye anati kwa Iye, Mphunzitsi, zonsezi ndinazisunga kuyambira ndili mwana.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anati, “Aphunzitsi zonsezi ndinazisunga kuyambira ndili mnyamata.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye anati kwa Iye, Mphunzitsi, zonsezi ndinazisunga kuyambira ndiri mwana.