Mark 10:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nkwapafupi kuti ngamira idzere pa kachiboo ka zingano, kupambana kuti munthu wachuma akaloŵe mu Ufumu wa Mulungu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nkwa pafupi kuti ngamira ipyole diso la singano kuposa kuti mwini chuma alowe mu Ufumu wa Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi kwapafupi kwa ngamira kuti idzere pa kabowo ka zingano kusiyana ndi munthu wachuma kuti alowe mu ufumu wa Mulungu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nkwa pafupi kuti ngamila ipyole diso la singano koposa kuti mwini cuma alowe mu Ufumu wa Mulungu.