Mark 10:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo adati, “Mose adalola kuti munthu azilembera mkazi wake kalata yachisudzulo kenaka nkumuchotsa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati, Mose analola kulembera kalata wakulekanira, ndi kumchotsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anati, “Mose amaloleza mwamuna kulemba kalata ya chisudzulo ndi kumuchotsa mkazi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati, Mose analola kulembera kalata wakulekanira, ndi kumcotsa.