Mark 10:43 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma pakati pa inu zisamatero ai. Aliyense wofuna kukhala mkulu pakati panu, azikhala mtumiki wanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mwa inu sikutero ai; koma amene aliyense afuna kukhala wamkulu mwa inu adzakhala mtumiki wanu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sizili choncho ndi inu. Mʼmalo mwake, amene akufuna kukhala wamkulu pakati panu ayenera kukhala wotumikira,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mwa inu sikutero ai; kama amene ali yense afuna kukhala wamkuru mwa inu adzakhala mtumiki wanu;