Mark 10:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komatu pachiyambi paja, pamene Mulungu adalenga zonse, adaŵalenga anthu, wina wamwamuna wina wamkazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma kuyambira pa chiyambi cha malengedwe anawapanga mwamuna ndi mkazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma pachiyambi cha chilengedwe, Mulungu ‘analenga iwo, mwamuna ndi mkazi.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma kuyambira pa ciyambi ca malengedwe anawapanga mwamuna ndi mkazi.