Mark 10:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake mwamuna azisiya atate ndi amai, nakaphatikizana ndi mkazi wake,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake mwamuna adzasiya atate wake ndi amai wake, ndipo adzaphatikizana ndi mkazi wake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
‘Pa chifukwa ichi mwamuna adzasiya abambo ake ndi amayi ake nakaphatikana ndi mkazi wake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace mwamuna adzasiya atate wace ndi amai wace, ndipo adzaphatikizana ndi mkazi wace;