Mark 11:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ataona mkuyu chapatali potero, uli ndi masamba, adapitapo kuti kapena nkupezamo nkhuyu. Koma atafika, sadapezemo nkhuyu, koma masamba okhaokha, pakuti siinali nyengo ya nkhuyu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anaona mkuyu kutali, uli ndi masamba; ndipo anadza Iye, kuti kapena akapezapo kanthu: ndipo m'mene anafikako anapeza palibe kanthu koma masamba okha; pakuti siinali nyengo yake ya nkhuyu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ataonera patali mtengo wamkuyu uli ndi masamba, anapita kuti akaone ngati unali ndi chipatso chilichonse. Atafika, sanapezemo kanthu koma masamba, chifukwa sinali nthawi ya nkhuyu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaona mkuyu kutali, uli ndi masamba; ndipo anadza Iye, kuti kapena akapezapo kanthu: ndipo m'mene anafikako anapeza palibe kanthu koma masamba okha; pakuti siinali nyengo yace ya nkhuyu.