Mark 11:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'maŵa mwake, m'mamaŵa ndithu, iwo akuyenda mu mseu, adaona mkuyu uja waumiratu wonse ndi mizu yomwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'mene anapitapo m'mawa mwake, anaona kuti mkuyu uja unafota, kuyambira kumizu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mmamawa, pamene ankayenda, anaona mtengo wamkuyu uja utafota kuyambira ku mizu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'mene anapitapo m'mawa mwace, anaona kuti mkuyu uja unafota, kuyambira kumizu.