Mark 11:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komanso tikati adaazitenga kwa anthu, apo ndiye ainso.” Adaatero chifukwa choopa anthu, pakuti anthu onse ankati Yohane anali mneneri weniweni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma tikati, Kwa anthu, anaopa anthuwo; pakuti onse anamuyesa Yohane mneneri ndithu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ife tikati, ‘Wochokera kwa anthu.’ ” (Amaopa anthu, pakuti aliyense amakhulupirira kuti Yohane analidi mneneri).
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma tikati, Kwa anthu —anaopa anthuwo; pakuti onse anamuyesa Yohane mneneri ndithu.