Mark 11:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu amene adaali pamenepo adaŵafunsa kuti, “Inu nchiyani chimenecho, buluyo mukummasuliranji?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ena akuima kumeneko ananena nao, Muchita chiyani ndi kumasula mwana wa bulu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
anthu ena amene anayima pomwepo anafunsa kuti, “Mukuchita chiyani, kumasula mwana wabuluyo?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ena akuima kumeneko ananena nao, Mucita ciani ndi kumasula mwana wa buru?