Mark 11:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ambiri ankayala zovala zao mu mseu, ena nkumayalika nthambi zamasamba zomwe ankakazithyola ku thengo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndimo ambiri anayala zovala zao panjira; ndi ena zitsamba, anazidula m'minda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu ambiri anayala mikanjo yawo pa msewu, pamene ena anayala nthambi zomwe anadula mʼminda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndimo ambiri anayala zobvala zao panjira; ndi ena zitsamba, anazidula m'minda.