Mark 12:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ena a m'gulu la Afarisi, ndi enanso a m'chipani cha Herode, adaatumidwa kuti akatape Yesu m'kamwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatuma kwa Iye ena a Afarisi ndi a Aherode, kuti akamkole Iye m'kulankhula kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pambuyo pake anatuma ena a Afarisi ndi Aherode kwa Yesu kuti adzamukole mawu ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anatuma kwa Iye ena a Afarisi ndi a Aherode, kuti akamkole Iye m'kulankhula kwace.