Mark 12:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Asaduki ena adadza kwa Yesu. Iwo amati akufa sadzauka. Adamufunsa kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anadza kwa Iye Asaduki, amene amanena kuti palibe kuuka kwa akufa; ndipo anamfunsa Iye, nanena,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Asaduki, amene amati kulibe kuuka kwa akufa, anabwera kwa Iye ndi funso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anadza kwa Iye Asaduki, amene amanena kuti palibe kuuka kwa akufa; ndipo anamfunsa Iye, nanena,