Mark 12:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono padaali anthu asanu ndi aŵiri pachibale pao. Woyamba adaakwatira mkazi, namwalira opanda mwana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Analipo abale asanu ndi awiri; woyamba anakwatira mkazi, nafa, wosasiya mbeu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano panali abale asanu ndi awiri. Woyamba anakwatira namwalira wosabereka ana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Analipo abale asanu ndi awiri; woyamba anakwatira mkazi, nafa, wosasiya mbeu;