Mark 12:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wachiŵiri adamtenga mai uja, nayenso nkumwalira osasiya mwana. Wachitatunso chimodzimodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo wachiwiri anamkwatira, nafa, wosasiya mbeu; ndipo wachitatunso anatero momwemo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wachiwiri anakwatira mkazi wamasiyeyo, koma iye anamwalira wosabereka mwana. Zinali chimodzimodzi ndi wachitatu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo waciwiri anamkwatira, nafa, wosasiya mbeu; ndipo wacitatunso anatero momwemo;