Mark 12:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye kutitu sali Mulungu wa anthu akufa ai, koma wa anthu amoyo. Inu ndinu olakwa kwabasi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sali Mulungu wa akufa, koma wa amoyo: musochera inu ndithu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye si Mulungu wa anthu akufa, koma wa amoyo. Inu mwalakwitsa kwambiri!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sali Mulungu wa akufa, koma wa amoyo: musocera inu ndithu.