Mark 12:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Yesu ankaphunzitsa anthu m'Nyumba ya Mulungu, adafunsa kuti, “Kodi bwanji aphunzitsi a Malamulo amati Mpulumutsi wolonjezedwa uja ndi mwana wa Davide?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yesu pamene anaphunzitsa m'Kachisi, anayankha, nanena, Bwanji alembi anena kuti Khristu ndiye mwana wa Davide?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yesu akuphunzitsa mʼmabwalo a Nyumba ya Mulungu, anafunsa kuti, “Nʼchifukwa chiyani aphunzitsi amalamulo amanena kuti, ‘Khristu ndi Mwana wa Davide?’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yesu pamene anaphunzitsa m'Kacisi, anayankha, nanena, Bwanji alembi anena kuti Kristu ndiye mwana wa Davide?