Mark 12:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu uja adatumanso wantchito wina, koma alimi aja adamtema m'mutu nkumunyazitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatumanso kapolo wina kwa iwo; ndipo ameneyu anamlasa mutu, namchitira zomchititsa manyazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anatumizanso wantchito wina kwa iwo. Iwo anamumenya munthuyo pamutu ndipo anamuzunza mochititsa manyazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anatumanso kapolo wina kwa iwo; ndipo ameneyu anamlasa mutu, namcitira zomcititsa manyazi.