Mark 12:42 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma padafika mai wina wamasiye, wosauka. Iyeyu adangoponyamo tindalama tiŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anadza mkazi wamasiye waumphawi, ndipo iye anaponyamo tindalama tiwiri tating'ono tokwanira kakobiri kamodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mkazi wamasiye, wosauka anabwera ndi kuyikamo tindalama tiwiri ta kopala, tongokwanira theka la ndalama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anadza mkazi wamasiye waumphawi, ndipo iye anaponyamo tindalama tiwiri tanng'ono tofa kakobiri kamodzi.