Mark 12:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Munthu uja adangotsala ndi mmodzi basi, mwana wake weniweni wapamtima. Ndiye pambuyo pa onse adadzatuma iyeyu. Adati, ‘Mwana wanga yekhayu akamchitira ulemu.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anamtsalira mmodzi, ndiye mwana wake wokondedwa; potsiriza anamtuma iye kwa iwo, nanena, Adzamchitira ulemu mwana wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Munthu uja anatsala ndi mwana mmodzi, wamwamuna amene amamukonda. Pomaliza anamutumiza mwanayo nati, ‘Adzamuchitira ulemu mwana wanga.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anamtsalira mmodzi, ndiye mwana wace wokondedwa; potsiriza anamtuma iye kwa iwo, nanena, Adzamcitira ulemu mwana wanga.