Mark 12:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adamugwiradi, namupha nkumuponya kunja kwa mundawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamtenga, namupha iye, namtaya kunja kwa munda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anamutenga ndi kumupha, ndipo anamuponya kunja kwa munda wamphesa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamtenga, namupha iye, namtaya kunja kwa munda.