Mark 13:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amene ali padenga pa nyumba yake, asati atsike kuti akatenge chinthu m'nyumba mwakemo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi iye amene ali pamwamba pa chindwi asatsike, kapena asalowe kukatulutsa kanthu m'nyumba mwake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aliyense amene ali pa denga la nyumba yake asatsike kapena kulowa mʼnyumba kukatenga kanthu kalikonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi iye amene ali pamwamba pa chindwi asatsike, kapena asalowe kukaturutsa kanthu m'nyumba mwace;