Mark 13:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ali ndi tsoka akazi amene adzakhale ndi pathupi, ndiponso azimai oyamwitsa ana masiku amenewo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma tsoka iwo akukhala ndi pakati, ndi akuyamwitsa ana masiku awo!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kudzakhala koopsa mʼmasiku amenewo kwa amayi oyembekezera ndi amayi oyamwitsa!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma tsoka iwo akukhala ndi pakati, ndi akuyamwitsa ana masiku awol