Mark 13:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Pa nthaŵi imeneyo, wina akadzakuuzani kuti, ‘Ali panotu Khristu uja,’ kapena kuti, ‘Uyo ali apoyo,’ musadzakhulupirire.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamenepo wina akati kwa inu, Onani Khristu ali pano; kapena, Onani, uko; musavomereze;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nthawi imeneyo, ngati wina adzati kwa inu, ‘Taonani, Khristu ali kuno, kapena, Taonani, uyo ali apoyo!’ musakhulupirire.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamenepo wina akati kwa inu, Onani Kristu ali pano; kapena, Onani, uko; musabvomereze;