Mark 13:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Masiku amenewo, mavutowo atatha, dzuŵa lidzada, mwezi udzaleka kuŵala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma m'masikuwo, chitatha chisautso chimenecho, dzuwa lidzadetsedwa, ndi mwezi sudzapatsa kuunika kwake,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma masiku amenewo, masautsowo atatha, “ ‘dzuwa lidzada, ndipo mwezi sudzawala;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma m'masikuwo, citatha cisautso cimeneco, dzuwa lidzadetsedwa, ndi mwezi sudzapatsa kuunika kwace,