Mark 13:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Momwemonso mukadzaona zija ndanenazi zikuchitika, mudzadziŵe kuti Mwana wa Munthu ali pafupi, ali pakhomo penipeni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chomwecho inunso, pamene muona zinthu izi zilikuchitika, zindikirani kuti ali pafupi pakhomo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Momwenso pamene muona zinthu izi zikuchitika, dziwani kuti wayandikira, ali pa khomo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
comweco inunso, pamene muona zinthu izi zirikucitika, zindikirani kuti ali pafupi pakhomo.