Mark 13:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Yesu adakhala pansi, pa Phiri la Olivi, kuyang'anana ndi Nyumba ya Mulungu. Tsono Petro, Yakobe, Yohane ndi Andrea adamufunsa paokha, kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene anakhala Iye pa phiri la Azitona, popenyana ndi Kachisi, anamfunsa Iye m'tseri Petro, ndi Yakobo, ndi Yohane, ndi Andrea, kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yesu atakhala pansi pa phiri la Olivi moyangʼanana ndi Nyumba ya Mulungu, Petro, Yakobo, Yohane ndi Andreya anamufunsa Iye pambali kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene anakhala Iye pa phiri la Azitona, popenyana ndi Kacisi, anamfunsa Iye m'tseri Petro, ndi Yakobo, ndi Yohane, ndi Andreya, kuti,