Mark 13:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono chenjerani, khalani maso, chifukwa simudziŵa kuti nthaŵiyo idzakwana liti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yang'anirani, dikirani, pempherani: pakuti simudziwa nthawi yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Khalani maso! Khalani tcheru! Simudziwa pamene nthawi imeneyo idzafike.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yang'anirani, dikirani, pempherani: pakuti simudziwa nthawi yace.