Mark 13:37 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimene ndikunenazi, sindikuuza inu nokha ai, koma ndikuuza anthu onse kuti, ‘Khalani maso.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chimene ndinena ndi inu ndinena kwa onse, Dikirani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zimene ndikunena kwa inu, ndikunena kwa aliyense: ‘Khalani tcheru!’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo cimene ndinena ndi inu ndinena kwa onse, Dikirani.