Mark 14:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ankati, “Zimenezi tisadzachite pa nthaŵi ya chikondwerero ai, pangadzachitike chipolowe pakati pa anthu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti anati, Pachikondwerero ai, kuti pangakhale phokoso la anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anati, “Koma osati nthawi yaphwando, chifukwa anthu angachite chiwawa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti anati, Paphwando ai, kuti pangakhale phokoso la anthu.