Mark 14:51 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mnyamata wina ankatsatira Yesu, atangofundira nsalu yokha, opanda chovala china. Anthu aja adaati amgwire,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mnyamata wina anamtsata Iye, atafundira pathupi bafuta yekha; ndipo anamgwira;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mnyamata wamngʼono amene anangofundira nsalu yokha, wopanda chovala ankamutsatira Yesu. Atamugwira,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mnyamata wina anamtsata Iye, atapfundira pathupi bafuta yekha; ndipo anamgwira;