Mark 14:57 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ena adaimirira nayamba kumneneza zabodza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ananyamukapo ena, namchitira umboni wakunama, nanena kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka ena anayimirira namunenera umboni wonama womutsutsa Iye kunena kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ananyamukapo ena, namcitira umboni wakunama, nanena kuti,