Mark 14:63 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo mkulu wa ansembe uja adang'amba zovala zake, nati, “Kodi pamenepa tikusoŵanso mboni zina?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mkulu wa ansembe anang'amba malaya ake, nanena, Tifuniranjinso mboni zina?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mkulu wa ansembe anangʼamba zovala zaunsembe zake. Iye anafunsa kuti, “Chifukwa chiyani tikufuna mboni zinanso?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mkulu wa ansembe anang'amba maraya ace, nanena, Tifuniranjinso mboni zina?