Mark 14:68 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Petro adakana, adati, “Zimenezo ine sindikuzidziŵa, sindikuzimvetsa konse.” Ndipo adatuluka kumapita cha ku chipata. Pamenepo tambala adalira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anakana, nanena, Sindidziwa kapena kumvetsa chimene uchinena iwe; ndipo anatuluka kunka kuchipata; ndipo tambala analira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma iye anakana nati, “Sindikudziwa kapena kumvetsetsa zimene ukuyankhula.” Ndipo anachoka napita ku chipata.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anakana, nanena, Sindidziwa kapena kumvetsa cimene ucinena iwe; ndipo anaturuka kunka kucipata; ndipo tambala analira.