Mark 14:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iyeyu wachita zimene akadatha kuchita. Wadzozeratu thupi langa ndi mafuta onunkhira, kuti alikonzeretu lisanaikidwe m'manda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye wachita chimene wakhoza; anandidzozeratu thupi langa ku kuikidwa m'manda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wachita zimene akanatha. Wathira mafuta onunkhira pa thupi langa nthawi isanakwane kukonzekera kuyikidwa kwanga mʼmanda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye wacita cimene wakhoza; anandidzozeratu thupi langa ku kuikidwa m'manda.