Mark 15:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaatero chifukwa adaadziŵa kuti Yesuyo akulu a ansembewo angodzampereka chifukwa cha kaduka chabe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti anazindikira kuti ansembe aakulu anampereka Iye mwanjiru.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
podziwa kuti akulu a ansembe anamupereka Yesu kwa iye chifukwa cha nsanje.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti anazindikira kuti ansembe akuru anampereka Iye mwanjiru.