Mark 15:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma akulu a ansembewo adasonkhezera anthu onse aja kuti apemphe kuŵamasulira Barabasi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ansembe aakulu anasonkhezera khamulo, kuti makamaka awamasulire Barabasi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma akulu a ansembe anasonkhezera anthu kuti Pilato amasule Baraba mʼmalo mwa Yesu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ansembe akuru anasonkezera khamulo, kuti makamaka awamasulire Baraba.