Mark 15:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamuveka chovala chofiirira, naluka nsangamutu yaminga nkuiika pamutu pake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamveka Iye chibakuwa, naluka korona waminga, namveka pa Iye;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anamuveka Iye mwinjiro wofiira, kenaka analuka chipewa cha minga ndi kuyika pa mutu pake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anambveka Iye cibakuwa, naluka korona waminga, nambveka pa Iye;