Mark 15:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka adayamba kumampatsa moni kuti, “Tikuwoneni, mfumu ya Ayuda.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anayamba kumlankhula Iye, kuti, Tikuoneni, mfumu ya Ayuda!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anayamba kunena kwa lye kuti, “Ulemu kwa inu Mfumu ya Ayuda!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo anayamba kumlankhula Iye, kuti, Tikuoneni, Mfumu ya Ayuda!