Mark 15:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaafuna kumpatsa vinyo wosanganiza ndi mure kuti amwe, koma Iye adakana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anampatsa vinyo wosanganiza ndi mure; koma Iye sanamlandire.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anamupatsa Iye vinyo wosakaniza ndi mure, koma Iye sanamwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anampatsa vinyo wosanganiza ndi mure; koma Iye sanamlandira.